Ndimangofuna Ungondilora

Ndimangofuna Ungondilora

Tricky ayee Eeeeh Desho Desho Zoona zake ndiwe wokongola Ndipo ulusi umawusosola Kuwona kwanu kweko nkwa ndalama Kuwona level yako yapamwamba I have been lying lying lying to you I have been lying lying lying to you Zoti ndine Nurse doctor ayee Ndinkangokamba for you to accept Ntchito yanga yeniyeni ndiyokolopa Ntchito yanga yeniyeni ndiyosesa Zonse zija ine nkangokamba Ncholinga choti iweyo uvomere Oh wuh woh oh oh Ndimangofuna ungondilora Ndimangofuna ukhale wanga Ndimangofuna ungondilora Nchifukwa chake nnakunamiza Ndimangofuna ungondilora Ndimangofuna ukhale wanga Ndimangofuna ungondilora Nchifukwa chake nnakunamiza I used to buy things from my friends To make you comfortable and impressed Nnayiwala kuti chowuluka chimatera Nkhani zobisika zija wazitolera Besides the lie I told you Ayeee Eeeh You are the one I want I loooo I care Ntchito yanga ndiyokolopa Ntchito yanga ndiyosesa Ntchito yanga ndiyotchetcha Ndimangofuna undilore Undilore iwe undilore Oh wuh woh oh oh Ndimangofuna ungondilora Ndimangofuna ukhale wanga Ndimangofuna ungondilora Nchifukwa chake nnakunamiza Ndimangofuna ungondilora Ndimangofuna ukhale wanga Ndimangofuna ungondilora Nchifukwa chake nnakunamiza Eeeh Eh Eeh Eeeh Eeh Eeeh Eeeh Eh Eeh Eeeh Eeh Eeeh Eeeeeeh Ndimangofuna ungondilora Ndimangofuna ukhale wanga Ndimangofuna ungondilora Nchifukwa chake nnakunamiza Ndimangofuna ungondilora Ndimangofuna ukhale wanga Ndimangofuna ungondilora Nchifukwa chake nnakunamiza

Ndimangofuna Ungondilora

DESHO · 1678377600000

DESHO的其他专辑