Ye ye ye ye ye Yea oh yea Kumaufila ah kumaufila Kumaufila yea kumaufila Kumaufila yea kumaufila Kumaufila 'Umaufila Mavuto sazatha Osamangodanda moyowu Kumaufila kumaufila Mavuto sazatha Osamangodanda moyowu Kumaufila kumaufila Ngati moni lero Ndadzuka pa high Yea, Mbalame Swagga ndingofila fly Koma zodandaula lerolo ayi Ndasankha kusangalala Let me tell you why Nthawi zina Ndimapezeka ndakodwa Muzima stress Nkumakanika kukondwa Koma Lero lokha Nde sindingachite Kumandaula za ngini Yoti sindingasinthe Ya Ndati lero uh uh Yea lero palibe Nkhani zodanda Akakhala ma stress Ndikungogwanda Zikakhala nkhawa Chimwemwe Changa sizikulanda Yah Ndili ndi Zifukwa zomasekelera Zisomo za sefukila Z'uchita kuyendelera Yea moyo ndi kamodzi Nde osamangodanda Kumaufila boss Kumaufila 'Umaufila Mavuto sazatha osamangodanda Moyowu kumaufila kumaufila Why I gotta worry Why I gotta stress Life is what you make it My brother it's all finesse Lero siz'uyenda mawa zikubang'a It's a happy people always 'khalangati Tana It's all about perspective Osamazipatsa busy One step at a time my brother Gotta take it easy Yea I hear my enemies Are praying for my down fall But my God got an umbrella For every down pour Standing ovation My life is like an encore Happiness yanga Ndimagula chi bundle Kusaka zi dola The bag I never fumble Ikakhala nkhani yofila Am in the front bro A mathematician Ama count all my blessings It's never losses My brother its only lessons Am God gifted my mind Lifted am on a wave Ngati pali plan yofila Tell em am on the way Kumaufila 'Umaufila Mavuto sazatha Osamangodanda Moyowu kumaufila Kumaufila Moyowu ndi ophweka Osaulimbitsa Zisangalalo zambiri salipilitsa Ufulu ndi chuma usamautchipitsa Nde nthawi ina yake Moyo kumaufilitsa Mavuto ena Sungakwanitse kuthawa Ukazithawa lero Zimabwera mawa Moyo umabwera Ndi zake zopinga Moyo ndi choncho Sipalepheranso minga Yea uh kunjoya ndi ulere Olo ngini low Koma mahape mmalere Olo ngini ingapenge Sindimadanda Ndimadziwa zonse ndikhenge Ya kumaufila kumaufila Ndipo ukuyenera kuzindikira Mavuto sadzatha Lero ukulira Mawa kusekelera Moyo nkumapitilira Kumaufila 'Umaufila Mavuto sazatha osamangodanda Moyowu kumaufila, kumaufila
S.A.M.U.E.L的其他专辑
- 1695916800000