Oh yeah yeah yeah Desho man once again Chuluke chuluke inded ndiwanjuchi Umanena yomwe yakuluma Ndasiya kulira kuwona zokhoma Chifukwa Cha chikondi chako chokoma Sindimadziwa ndingamupeze Mkazi wokongola ngati iwe eeeh Sindimadziwa ndingamupeze Mkazi wokonda ngati iwe Oh my oh my my baby oh my Oh my oh my my baby Unkachedwa kuti weeh Unali kuti honey Ndichikondi chakochi Unkachedwa kuti Ndichikondi chako chokoma Chikondi koma ichi Kwina kuja ndinkangochedwa Chikondi koma ichi Kwina kuja ndinkadzichedwetsa Oh yeah yeah Zokwiyakwiya si mbali yako Baby ndisaname Zomveramverazi si mbali yako Baby ndisaname Akanakhala wina Bwez atathawa kale Zinthuso zikavuta Ndiwe amene undilimbitsa mtima Oh my oh my my baby oh my Oh my oh my my baby Unkachedwa kuti weeh Unali kuti honey Ndichikondi chakochi Unkachedwa kuti Ndichikondi chako chokoma Chikondi koma ichi Kwina kuja ndinkangochedwa Chikondi koma ichi Kwina kuja ndinkadzichedwetsa Oh yeah yeah Koma ichi Chikondi koma ichichi Koma ichi Chikondi koma ichichi Koma ichi Koma ichi Chokoma ichi Chikondi koma ichichi (Unali kuti honey Ndichikondi chakochi Unkachedwa kuti Ndichikondi chako chokoma Chikondi koma ichi Kwina kuja ndinkangochedwa Chikondi koma ichi Kwina kuja ndinkadzichedwetsa Oh yeah yeah) Ah yeah yeah Desho Desho Ah yeah Tricky eeh Vikweshekweshe Iih yeah eh eeh aah yeah yeah yeah
DESHO的其他专辑
- 1679846400000
- 1678377600000
- 1678377600000
- 1678377600000
- 1678377600000
- 1678377600000
- 1678377600000