Yeah Dj sai Me again Ebel Yeah iwe ndi duwa losafota Uli ngat kaganja kosapota Ndapenga nawe moti ndili zomba Mental ndakwera instrumental Ndigula plot mumtima mwakomo Sindikufuna kupeya rent Ndimamukonda for real Sizongopanga pretend Chikondi chathu cha daily 1 mpaka month end Kuwala kwako ndi one Our love will never end I will treat good Baeb sudzasowa food Ndikuthokazi sizandudu Sinzakuthira makhatcha majudu Ndikuthokazi sizandudu Sinzakuthira makhatcha majudu Ndiwe wokongola ngati kaduwa Sindikuyimva ndikutengera paguwa Tabwera tabwera iwe honey taponya sitepe Ngakhale ma hater aname sindingakuleke Ndiwe future future future ya ine Ndiwe dzuwa lowalira dziko la ine Oyesa kulanda kumusiyira dzino Kumuluma ngat chi vampaya Osasekera kumgwira pa khosi Kumusenda ngat chi pampaya Chikndi timachifera ngat mtembo Kuzerezeka nacho ngat bengo Ndi mmene unakongolera Or chitsiru chikhoza kukhala ndi mphamvu Kuwala kwako ndi chiletso mami Mkazi wa nzeru ndasankha iwe honey Kusiya iwe ndingalowere kwani Sindizalora kukudyetsa nkhwani Ife timakhalana tisapange zibwana Palibe kusiyana palibe zomenyana Ndiwe wokongola ngati kaduwa Sindikuyimva ndikutengera paguwa Tabwera tabwera iwe honey taponya sitepe Ngakhale ma hater aname sindingakuleke Ndiwe future future future ya ine Ndiwe dzuwa lowalira dziko la ine Ndiwe wokongola ngati kaduwa Sindikuyimva ndikutengera paguwa Tabwera tabwera iwe honey taponya sitepe Ngakhale ma hater aname sindingakuleke Ndiwe future future future ya ine Ndiwe dzuwa lowalira dziko la ine
Ebel的其他专辑
- 1694707200000
- 1688054400000
- 1683388800000
- 1683388800000
- 1683302400000
- 1683216000000
- 1683216000000
Gaxybo的其他专辑
- 1683216000000