Delilah

Delilah

Oowoooo Ebel Nanananana Mr Shine Iwe beibe ndiwe okongola kufanana iwe ndi Delilah nkhope yokongola iwe Ukamamwetulira iwe beibe tima dimples nso nkuchimake ayi ndakukonda iwe Iwe beibe ndiwe okongola kufanana iwe ndi Delilah nkhope yokongola iwe Eeeh yeaaah aaaah Beibe uuuummmh Aaahaa Ndiwe okongola Nzanga ndiwe nthiti yanga ndiwee aaaaah Usanamizidweee I will never leave you aaaah Usaganize zanu filimu izi Zamu filimu Koma izi nzenizeni Usazitenge zama sewera izi zamasewera Ayi chikondi chenicheni Beibe iwe ndi ine ndithu tikudyerera Tili awiriwiriwiri tiku mwerera Iwe ndiine beibe bri bri bri Then makes our life easier Beibe ndikudziwa kuti umandikonda and I promise kuti sudzawonda And I promise kuti sudzawonda Iwe ndi ine beibe bri bri bri Vuma vuma Ntombi yemhlophe Vuma Vuma ubengowami Vuma sibe moya omunye vuma nkanyezi yokusa Vuma vuma Ntombi yemhlophe Vuma Vuma ubengowami Vuma sibe moya omunye vuma nkanyezi yokusa Nzanga ndiwe nthiti yanga ndiwee aaaaah Usanamizidweee I will never leave you aaaah Usaganize zanu filimu izi Zamu filimu Koma izi nzenizeni Usazitenge zama sewera izi zamasewera Ayi chikondi chenicheni Nzanga ndiwe ooowyahh Nthiti yanga ndiwee beibe Wanga ndiwe beibe Usanamizidwe eeeyeah I will never leave you ooowyeah aaaah Usaganize zamu filimu izi zamu filimu Koma izi ndizenizeni Usazitenge zama sewera izi zamasewera ayi chikondi chenicheni

Delilah

Ebel · 1683216000000

1

Ebel的其他专辑